On AG Thabo Chakaka Nyirenda and his style to silence doubters

One thing I love about the AG Thabo Chakaka is that when he is about to do something, we always feel its impossible, sizingatheke, ndipo amatukwanidwa. Kenako timangomva ati watchaya wagwetsa uku. Wawina.

And, sakonda zoyankhula yankhula even akamawina, komanso sanandaula kwambiri zikamamvuta. Timangomva kuti zikutheka uku, boma likusadabuza mbamva, milandu akuwina, ndalama za nkhani nkhani zikupulumuka.

Ena ake anawasiyila 16 mita atapanga claim ma 100s of millions. Imene ija ndimaseka mpaka lero.

When he brought the issue of Amnesty, tikanangomusiya. Anali atawona zomwe inu ndi ine sitinawone. Koma tinamutukwana munthu, kumutsukuluza, kumuphunzitsa malamulo, ena mpaka kumutchula zobisika.

Pa Amnesty paja I think tikanawinapo tikanamusiya.

Munthu uyu anawona kuti zinazo zivutilapo sizingatheke chifukwa ndi chi chain chamaulamuliro, ma department, ma business, ma crook, etc. Koma anthu timayankhulitsa. Sometimes we behave like we are all lawyers pa Facebook pano.

But kudos to the AG. Ofcourse he will end up being the most pooresr AG, ever, but what would benefit him to gain the whole world and lose his soul?

I will frame a picture of Thabo Chakaka in my house. You will see him when you visit me.

2 thoughts on “On AG Thabo Chakaka Nyirenda and his style to silence doubters

  1. Bernard PM Kawonga

    Kudos to the AG

  2. Agness

    He is the best

What do you think about this topic?

Recommended Posts

Cookies Notice

This site uses cookies so that we can remember you and understand how you use our site. You can change this message and links below in your site.

Please Read Our Cookies Privacy Policies

I Agree
%d bloggers like this: